Deuteronomo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 samala kuti usaiwale+ Yehova amene anakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo. 1 Samueli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno munthu wa Mulungu+ anapita kwa Eli ndi kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinadzisonyeze kunyumba ya kholo lako pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+
27 Ndiyeno munthu wa Mulungu+ anapita kwa Eli ndi kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinadzisonyeze kunyumba ya kholo lako pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+