Ekisodo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anatenga mawu a anthuwo ndi kubwerera nawo kwa Yehova.+ Yoswa 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova anathamangitsa mitundu yonse ya anthu+ pamaso pathu, ngakhale Aamori amene anali kukhala m’dzikoli. Choncho, nafenso tizitumikira Yehova chifukwa iye ndi Mulungu wathu.”+ Yesaya 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uyu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Uyo adzadzitcha dzina la Yakobo,+ ndipo wina adzalemba padzanja lake kuti: “Wa Yehova.” Munthu winanso adzadzipatsa dzina la Isiraeli.’+
8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anatenga mawu a anthuwo ndi kubwerera nawo kwa Yehova.+
18 Yehova anathamangitsa mitundu yonse ya anthu+ pamaso pathu, ngakhale Aamori amene anali kukhala m’dzikoli. Choncho, nafenso tizitumikira Yehova chifukwa iye ndi Mulungu wathu.”+
5 Uyu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Uyo adzadzitcha dzina la Yakobo,+ ndipo wina adzalemba padzanja lake kuti: “Wa Yehova.” Munthu winanso adzadzipatsa dzina la Isiraeli.’+