-
Yoswa 24:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Yehova anathamangitsa mitundu yonse ya anthu pamaso pathu, kuphatikizapo Aamori amene ankakhala mʼdzikoli. Choncho nafenso tipitiriza kutumikira Yehova chifukwa iye ndi Mulungu wathu.”
-