Oweruza 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yoswa atauza anthuwo kuti apite, aliyense wa ana a Isiraeliwo anapita ku cholowa chake, kukatenga dzikolo kukhala lawo.+
6 Yoswa atauza anthuwo kuti apite, aliyense wa ana a Isiraeliwo anapita ku cholowa chake, kukatenga dzikolo kukhala lawo.+