Numeri 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘“Komanso, ana anu amene munati adzatengedwa ndi adani,+ nawonso ndidzawalowetsa m’dzikolo ndithu. Moti dziko limene inuyo mwalikana, iwo adzalidziwa bwino.+ Deuteronomo 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ana anu amene munanena kuti: “Adzagwidwa ndi adani!”+ ndiponso ana anu aang’ono amene lero sakudziwa chabwino kapena choipa, amenewa ndiwo adzalowa m’dziko limenelo. Amenewa ndidzawapatsa dzikolo ndipo adzalitenga kukhala lawo.
31 “‘“Komanso, ana anu amene munati adzatengedwa ndi adani,+ nawonso ndidzawalowetsa m’dzikolo ndithu. Moti dziko limene inuyo mwalikana, iwo adzalidziwa bwino.+
39 Koma ana anu amene munanena kuti: “Adzagwidwa ndi adani!”+ ndiponso ana anu aang’ono amene lero sakudziwa chabwino kapena choipa, amenewa ndiwo adzalowa m’dziko limenelo. Amenewa ndidzawapatsa dzikolo ndipo adzalitenga kukhala lawo.