Deuteronomo 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Deuteronomo 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usapatuke pa mawu onse amene ndikukulamula lero, kupita kudzanja lamanja kapena lamanzere+ kuti utsatire milungu ina ndi kuitumikira.+
32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
14 Usapatuke pa mawu onse amene ndikukulamula lero, kupita kudzanja lamanja kapena lamanzere+ kuti utsatire milungu ina ndi kuitumikira.+