Numeri 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa mpingowo nʼkupita kukhomo la chihema chokumanako. Kumeneko, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi, ndipo ulemerero wa Yehova unayamba kuonekera kwa iwo.+
6 Zitatero Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa mpingowo nʼkupita kukhomo la chihema chokumanako. Kumeneko, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi, ndipo ulemerero wa Yehova unayamba kuonekera kwa iwo.+