Ekisodo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+ Yoswa 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero, anthu onse a mumzindawo anaitanidwa kuti akathamangitse Aisiraeli. Anthuwo anathamangitsa Aisiraeliwo limodzi ndi Yoswa, mpaka anafika kutali ndi mzinda wawo.+
9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+
16 Zitatero, anthu onse a mumzindawo anaitanidwa kuti akathamangitse Aisiraeli. Anthuwo anathamangitsa Aisiraeliwo limodzi ndi Yoswa, mpaka anafika kutali ndi mzinda wawo.+