Yoswa 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mamawa kutacha, Yoswa ndi ana a Isiraeli onse ananyamuka ku Sitimu.+ Anayenda mpaka kukafika kumtsinje wa Yorodano, kumene anagona usiku umenewo asanawoloke. Yoswa 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsiku lotsatira, Yoswa anadzuka m’mawa kwambiri,+ ndipo ansembe ananyamula likasa+ la Yehova.
3 M’mamawa kutacha, Yoswa ndi ana a Isiraeli onse ananyamuka ku Sitimu.+ Anayenda mpaka kukafika kumtsinje wa Yorodano, kumene anagona usiku umenewo asanawoloke.