Yoswa 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anawalamula kuti: “Inu mukabisale+ kumbuyo kwa mzindawo. Musakakhale patali kwambiri ndi mzindawo, ndipo nonsenu mukakhale okonzeka.
4 Anawalamula kuti: “Inu mukabisale+ kumbuyo kwa mzindawo. Musakakhale patali kwambiri ndi mzindawo, ndipo nonsenu mukakhale okonzeka.