Ekisodo 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, Mose akangokweza dzanja lake m’mwamba, Aisiraeli anali kupambana pankhondoyo,+ koma akangotsitsa dzanja lake, Aamaleki anali kupambana. Yoswa 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zikakatero, inu mukavumbuluke ndi kukalanda mzindawo, pakuti Yehova Mulungu wanu adzaupereka ndithu m’manja mwanu.+ Yoswa 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo Yoswa sanatsitse mkono wake umene anautambasula polozetsa nthungo+ kumzindawo, mpaka anthu onse a ku Ai ataphedwa.+
11 Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, Mose akangokweza dzanja lake m’mwamba, Aisiraeli anali kupambana pankhondoyo,+ koma akangotsitsa dzanja lake, Aamaleki anali kupambana.
7 Zikakatero, inu mukavumbuluke ndi kukalanda mzindawo, pakuti Yehova Mulungu wanu adzaupereka ndithu m’manja mwanu.+
26 Ndipo Yoswa sanatsitse mkono wake umene anautambasula polozetsa nthungo+ kumzindawo, mpaka anthu onse a ku Ai ataphedwa.+