Ekisodo 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, Mose akangokweza dzanja lake m’mwamba, Aisiraeli anali kupambana pankhondoyo,+ koma akangotsitsa dzanja lake, Aamaleki anali kupambana. Yoswa 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Lozetsa nthungo* imene ili m’dzanja lako ku Ai,+ pakuti mzindawo ndaupereka m’manja mwako.”+ Chotero Yoswa analozetsa kumzindawo nthungo imene inali m’dzanja lake.
11 Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, Mose akangokweza dzanja lake m’mwamba, Aisiraeli anali kupambana pankhondoyo,+ koma akangotsitsa dzanja lake, Aamaleki anali kupambana.
18 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Lozetsa nthungo* imene ili m’dzanja lako ku Ai,+ pakuti mzindawo ndaupereka m’manja mwako.”+ Chotero Yoswa analozetsa kumzindawo nthungo imene inali m’dzanja lake.