Yoswa 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukachite kwa Ai ndi mfumu yake zimene unachita kwa Yeriko ndi mfumu yake.+ Koma katundu ndi ziweto za mumzindawo mukafunkhe zikakhale zanu.+ Usankhe amuna ena oti akabisale kumbuyo kwa mzindawo.”+ Oweruza 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Isiraeli anaika amuna kuti abisalire+ mzinda wonse wa Gibeya.
2 Ukachite kwa Ai ndi mfumu yake zimene unachita kwa Yeriko ndi mfumu yake.+ Koma katundu ndi ziweto za mumzindawo mukafunkhe zikakhale zanu.+ Usankhe amuna ena oti akabisale kumbuyo kwa mzindawo.”+