Yoswa 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anawalamula kuti: “Inu mukabisale+ kumbuyo kwa mzindawo. Musakakhale patali kwambiri ndi mzindawo, ndipo nonsenu mukakhale okonzeka. 1 Samueli 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako, Sauli anafika kumzinda wa Amaleki ndi kuubisalira kuchigwa.* Miyambo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+ Mlaliki 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndi bwino kukhala ndi nzeru kuposa kukhala ndi zida zomenyera nkhondo, ndipo wochimwa mmodzi yekha akhoza kuwononga zabwino zochuluka.+
4 Anawalamula kuti: “Inu mukabisale+ kumbuyo kwa mzindawo. Musakakhale patali kwambiri ndi mzindawo, ndipo nonsenu mukakhale okonzeka.
6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+
18 Ndi bwino kukhala ndi nzeru kuposa kukhala ndi zida zomenyera nkhondo, ndipo wochimwa mmodzi yekha akhoza kuwononga zabwino zochuluka.+