Yoswa 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda 9, kuchokera m’mafuko awiri amenewa. 1 Samueli 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ng’ombezo zinayamba kuyenda, kulunjika msewu wa ku Beti-semesi.+ Zinali kuyenda pamsewu waukulu wopita kumeneko zikulira, ndipo sizinapatukire kudzanja lamanja kapena lamanzere. Apa n’kuti olamulira ogwirizana+ a Afilisiti akuzitsatira pambuyo mpaka kukafika m’malire a Beti-semesi. 2 Mafumu 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Amaziya sanamvere.+ Chotero Yehoasi, mfumu ya Isiraeli, anabwera, ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anamenyana+ ku Beti-semesi+ m’dziko la Yuda. 1 Mbiri 6:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 mzinda wa Asani+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto.
16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda 9, kuchokera m’mafuko awiri amenewa.
12 Ng’ombezo zinayamba kuyenda, kulunjika msewu wa ku Beti-semesi.+ Zinali kuyenda pamsewu waukulu wopita kumeneko zikulira, ndipo sizinapatukire kudzanja lamanja kapena lamanzere. Apa n’kuti olamulira ogwirizana+ a Afilisiti akuzitsatira pambuyo mpaka kukafika m’malire a Beti-semesi.
11 Koma Amaziya sanamvere.+ Chotero Yehoasi, mfumu ya Isiraeli, anabwera, ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anamenyana+ ku Beti-semesi+ m’dziko la Yuda.
59 mzinda wa Asani+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto.