Genesis 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye chifukwa chake iye anatcha malowo Beere-seba,+ chifukwa chakuti onse awiri analumbirirana pamalopo. Yoswa 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’gawo la cholowa chawo munali Beere-seba+ kuphatikizapo Sheba, Molada,+
31 Ndiye chifukwa chake iye anatcha malowo Beere-seba,+ chifukwa chakuti onse awiri analumbirirana pamalopo.