Genesis 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye chifukwa chake iye anatcha malowo Beere-seba,+ chifukwa chakuti onse awiri analumbirirana pamalopo. Genesis 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chotero chitsimecho anachitcha Siba.* Ndiye chifukwa chake dzina la mzindawo ndi Beere-seba,+ mpaka lero. Yoswa 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Hazara-suali,+ Beere-seba,+ Bizioti,
31 Ndiye chifukwa chake iye anatcha malowo Beere-seba,+ chifukwa chakuti onse awiri analumbirirana pamalopo.
33 Chotero chitsimecho anachitcha Siba.* Ndiye chifukwa chake dzina la mzindawo ndi Beere-seba,+ mpaka lero.