Yoswa 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zikilaga,+ Beti-marikaboti, Hazara-susa,+ 1 Samueli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Akisi anam’patsa mzinda wa Zikilaga+ pa tsiku limenelo. N’chifukwa chake mzinda wa Zikilaga wakhala wa mafumu a Yuda mpaka lero. 1 Mbiri 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano nawa anthu amene anapita kwa Davide ku Zikilaga,+ pa nthawi imene iye sanali kuyenda momasuka chifukwa choopa Sauli+ mwana wa Kisi. Iwowa anali ena mwa amuna amphamvu+ amene anamuthandiza pankhondo.
6 Choncho Akisi anam’patsa mzinda wa Zikilaga+ pa tsiku limenelo. N’chifukwa chake mzinda wa Zikilaga wakhala wa mafumu a Yuda mpaka lero.
12 Tsopano nawa anthu amene anapita kwa Davide ku Zikilaga,+ pa nthawi imene iye sanali kuyenda momasuka chifukwa choopa Sauli+ mwana wa Kisi. Iwowa anali ena mwa amuna amphamvu+ amene anamuthandiza pankhondo.