Nehemiya 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ku Zanowa,+ ku Adulamu+ ndi midzi yake yozungulira, ku Lakisi+ ndi madera ake ozungulira, ku Azeka+ ndi midzi yake yozungulira. Iwo anamanga misasa kuyambira ku Beere-seba mpaka kuchigwa cha Hinomu.+
30 ku Zanowa,+ ku Adulamu+ ndi midzi yake yozungulira, ku Lakisi+ ndi madera ake ozungulira, ku Azeka+ ndi midzi yake yozungulira. Iwo anamanga misasa kuyambira ku Beere-seba mpaka kuchigwa cha Hinomu.+