Yoswa 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anatsetserekera kumadzulo kumalire a Ayafeleti, mpaka kukafika kumalire a Beti-horoni Wakumunsi+ ndi Gezeri,+ n’kukathera kunyanja.+ Yoswa 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchoka ku Tapuwa,+ malirewo analowera chakumadzulo kuchigwa cha Kana+ n’kukathera kunyanja.+ Chimenechi ndi cholowa cha fuko la ana a Efuraimu potsata mabanja awo.
3 Kenako anatsetserekera kumadzulo kumalire a Ayafeleti, mpaka kukafika kumalire a Beti-horoni Wakumunsi+ ndi Gezeri,+ n’kukathera kunyanja.+
8 Kuchoka ku Tapuwa,+ malirewo analowera chakumadzulo kuchigwa cha Kana+ n’kukathera kunyanja.+ Chimenechi ndi cholowa cha fuko la ana a Efuraimu potsata mabanja awo.