Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Mundipangire Likasa la mtengo wa mthethe,+ mikono* iwiri ndi hafu m’litali, mkono umodzi ndi hafu m’lifupi, ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.

  • Yoswa 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako Yoswa anauza ansembe kuti: “Nyamulani likasa la pangano,+ muyende nalo patsogolo pa anthuwa.” Chotero ansembewo ananyamula likasa la panganolo, n’kumayenda nalo patsogolo pa anthuwo.

  • Machitidwe 7:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ndipo makolo athu amene anachilandira kwa makolo awo, analowa nacho limodzi ndi Yoswa,+ m’dziko limene linali m’manja mwa anthu a mitundu ina+ amene Mulungu anawapitikitsa pamaso pa makolo athu.+ Chihemacho chinakhala m’dziko limeneli mpaka m’masiku a Davide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena