Yoswa 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sankhani amuna atatu pafuko lililonse oti ndiwatume apite akayendere dzikolo. Akalembe mmene dzikolo lilili kuti lidzagawidwe monga cholowa cha mafuko awo, akakatero adzabwerere kwa ine.+
4 Sankhani amuna atatu pafuko lililonse oti ndiwatume apite akayendere dzikolo. Akalembe mmene dzikolo lilili kuti lidzagawidwe monga cholowa cha mafuko awo, akakatero adzabwerere kwa ine.+