Yoswa 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Gawo lawo linayambira ku Mahanaimu+ kuphatikizapo dera lonse la Basana,+ ndi dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi mfumu ya Basana, ndiponso midzi yonse ing’onoing’ono ya Yairi+ ku Basana. Gawo lawoli linali ndi matauni 60 onse pamodzi. 1 Mbiri 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Segubu anabereka Yairi,+ amene anadzakhala ndi mizinda 23+ m’dziko la Giliyadi.
30 Gawo lawo linayambira ku Mahanaimu+ kuphatikizapo dera lonse la Basana,+ ndi dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi mfumu ya Basana, ndiponso midzi yonse ing’onoing’ono ya Yairi+ ku Basana. Gawo lawoli linali ndi matauni 60 onse pamodzi.