Numeri 35:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Oweruzawo+ alanditse wakupha munthuyo m’manja mwa wobwezera magazi, ndipo am’bwezere kumzinda wothawirako kumene anathawira. Iye ayenera kukhala mumzindamo mpaka mkulu wa ansembe amene anadzozedwa ndi mafuta opatulika+ adzamwalire. Aheberi 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiponso, panayenera kukhala ansembe ambiri olowana m’malo+ chifukwa imfa+ inali kuwaletsa kupitiriza unsembe wawo.
25 Oweruzawo+ alanditse wakupha munthuyo m’manja mwa wobwezera magazi, ndipo am’bwezere kumzinda wothawirako kumene anathawira. Iye ayenera kukhala mumzindamo mpaka mkulu wa ansembe amene anadzozedwa ndi mafuta opatulika+ adzamwalire.
23 Ndiponso, panayenera kukhala ansembe ambiri olowana m’malo+ chifukwa imfa+ inali kuwaletsa kupitiriza unsembe wawo.