Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 17:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Aliyense anali kuchita zimene anali kuona kuti n’zoyenera.+

  • Oweruza 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndipo m’masiku amenewo fuko la Dani+ linali kufuna cholowa chake kuti likakhale kumeneko, chifukwa mpaka pa nthawi imeneyi linali lisanalandirebe cholowa pakati pa mafuko onse a Isiraeli.+

  • Oweruza 21:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Aliyense anali kuchita zimene anali kuona kuti n’zoyenera.+

  • 1 Samueli 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Patapita nthawi, akulu onse a mu Isiraeli+ anasonkhana pamodzi n’kupita kwa Samueli ku Rama.

  • 1 Samueli 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena