Genesis 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.” Salimo 104:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+ Miyambo 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu wopatsa mowolowa manja adzalandira mphoto,+ ndipo wothirira ena mosaumira nayenso adzathiriridwa mosaumira.+
5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”
15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+
25 Munthu wopatsa mowolowa manja adzalandira mphoto,+ ndipo wothirira ena mosaumira nayenso adzathiriridwa mosaumira.+