Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Madalitso+ a munthu amene watsala pang’ono kuwonongedwa ankabwera kwa ine,

      Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+

  • Yesaya 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma munthu wopatsa amapereka malangizo okhudza kupatsa, ndipo iyeyo amapitiriza kukhala wopatsa.+

  • Machitidwe 20:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 M’zinthu zonse ndakuonetsani kuti mwa kugwira ntchito molimbika chomwechi,+ muthandize ofookawo,+ ndipo muzikumbukira mawu a Ambuye Yesu. Pajatu iye anati, ‘Kupatsa kumabweretsa chimwemwe chochuluka+ kuposa kulandira.’”

  • 2 Akorinto 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma ponena za nkhaniyi, wobzala moumira+ adzakololanso zochepa, ndipo wobzala mowolowa manja+ adzakololanso zochuluka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena