Oweruza 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atafika kumzinda wa Gibeya, anapatuka kuti akalowe ndi kugona mmenemo. Ndiyeno analowa ndi kukhala pabwalo la mzindawo. Koma panalibe wowatenga kuti akagone m’nyumba yake.+
15 Atafika kumzinda wa Gibeya, anapatuka kuti akalowe ndi kugona mmenemo. Ndiyeno analowa ndi kukhala pabwalo la mzindawo. Koma panalibe wowatenga kuti akagone m’nyumba yake.+