Oweruza 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mdzakazi wakeyo anakhala wosakhulupirika kwa iye, moti anayamba kuchita dama.+ Pamapeto pake, mkaziyo anachoka n’kukakhala kwa bambo ake ku Betelehemu wa ku Yuda miyezi inayi yathunthu. Oweruza 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma amunawo sanafune kumumvera, moti Mleviyo anatenga mdzakazi wake+ ndi kum’pereka kwa amunawo kunja. Pamenepo, anthuwo anayamba kumugona,+ ndipo anapitiriza kum’zunza+ usiku wonse mpaka m’mawa. M’bandakucha anamusiya kuti apite.
2 Mdzakazi wakeyo anakhala wosakhulupirika kwa iye, moti anayamba kuchita dama.+ Pamapeto pake, mkaziyo anachoka n’kukakhala kwa bambo ake ku Betelehemu wa ku Yuda miyezi inayi yathunthu.
25 Koma amunawo sanafune kumumvera, moti Mleviyo anatenga mdzakazi wake+ ndi kum’pereka kwa amunawo kunja. Pamenepo, anthuwo anayamba kumugona,+ ndipo anapitiriza kum’zunza+ usiku wonse mpaka m’mawa. M’bandakucha anamusiya kuti apite.