Oweruza 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma amunawo sanafune kumumvera, moti Mleviyo anatenga mdzakazi wake+ ndi kum’pereka kwa amunawo kunja. Pamenepo, anthuwo anayamba kumugona,+ ndipo anapitiriza kum’zunza+ usiku wonse mpaka m’mawa. M’bandakucha anamusiya kuti apite.
25 Koma amunawo sanafune kumumvera, moti Mleviyo anatenga mdzakazi wake+ ndi kum’pereka kwa amunawo kunja. Pamenepo, anthuwo anayamba kumugona,+ ndipo anapitiriza kum’zunza+ usiku wonse mpaka m’mawa. M’bandakucha anamusiya kuti apite.