Oweruza 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amuna ogwira lupanga a mu Isiraeli amene anasonkhanitsidwa pamodzi anali 400,000,+ kupatulapo amuna a m’dera la Benjamini. Aliyense wa amenewa anali mwamuna wankhondo.
17 Amuna ogwira lupanga a mu Isiraeli amene anasonkhanitsidwa pamodzi anali 400,000,+ kupatulapo amuna a m’dera la Benjamini. Aliyense wa amenewa anali mwamuna wankhondo.