-
Oweruza 20:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Tsopano amuna a Isiraeli anapita kukamenyana ndi ana a Benjamini ku Gibeya, ndipo kumeneko amuna a Isiraeliwo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.
-
-
Oweruza 20:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma anthuwo, amuna a Isiraeli, analimba mtima ndipo anapitanso kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo pamalo omwe anafola tsiku loyamba lija.
-