Yoswa 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pofuna kuonetsa ngati akugonja, Yoswa limodzi ndi Aisiraeli onse amene anali naye+ anathawa kudzera njira yolowera kuchipululu.+
15 Pofuna kuonetsa ngati akugonja, Yoswa limodzi ndi Aisiraeli onse amene anali naye+ anathawa kudzera njira yolowera kuchipululu.+