Yoswa 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo, asilikali amene anabisala aja anavumbuluka pamalo pamene anali. Pa nthawi imene iye anatambasula dzanja lake, iwo anathamanga n’kukalowa mumzindawo n’kuulanda.+ Atatero, anauyatsa moto mzindawo mofulumira.+
19 Pamenepo, asilikali amene anabisala aja anavumbuluka pamalo pamene anali. Pa nthawi imene iye anatambasula dzanja lake, iwo anathamanga n’kukalowa mumzindawo n’kuulanda.+ Atatero, anauyatsa moto mzindawo mofulumira.+