Oweruza 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mukakaona ana aakazi a ku Silo akubwera kuti adzavine+ magule ovina mozungulira, mukavumbuluke m’minda ya mpesayo, ndipo aliyense akagwire mkazi mokakamiza pakati pa ana aakazi a ku Silo, ndi kupita nawo kudziko la Benjamini.
21 Ndiyeno mukakaona ana aakazi a ku Silo akubwera kuti adzavine+ magule ovina mozungulira, mukavumbuluke m’minda ya mpesayo, ndipo aliyense akagwire mkazi mokakamiza pakati pa ana aakazi a ku Silo, ndi kupita nawo kudziko la Benjamini.