Oweruza 20:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Amuna a Isiraeli anabwerera kukaukira ana a Benjamini ndipo anakantha ndi lupanga zonse za m’mizinda, kuyambira anthu mpaka ziweto, ndi chilichonse chimene anapeza.+ Kuwonjezera apo, mizinda yonse imene anaipeza anaiyatsa moto.+
48 Amuna a Isiraeli anabwerera kukaukira ana a Benjamini ndipo anakantha ndi lupanga zonse za m’mizinda, kuyambira anthu mpaka ziweto, ndi chilichonse chimene anapeza.+ Kuwonjezera apo, mizinda yonse imene anaipeza anaiyatsa moto.+