Yoswa 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anagawira cholowacho mafuko 9 ndi hafu, mwa kuchita maere,+ monga mmene Yehova analamulira kudzera mwa Mose.+ Oweruza 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yoswa atauza anthuwo kuti apite, aliyense wa ana a Isiraeliwo anapita ku cholowa chake, kukatenga dzikolo kukhala lawo.+ Oweruza 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo anthu onse ananyamuka mogwirizana,+ ndipo anati: “Aliyense wa ife sapitanso ku hema wake kapena kupatukira kunyumba yake.+
2 Anagawira cholowacho mafuko 9 ndi hafu, mwa kuchita maere,+ monga mmene Yehova analamulira kudzera mwa Mose.+
6 Yoswa atauza anthuwo kuti apite, aliyense wa ana a Isiraeliwo anapita ku cholowa chake, kukatenga dzikolo kukhala lawo.+
8 Pamenepo anthu onse ananyamuka mogwirizana,+ ndipo anati: “Aliyense wa ife sapitanso ku hema wake kapena kupatukira kunyumba yake.+