Oweruza 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Gidiyoni atangomva lotolo ndi tanthauzo lake,+ analambira Mulungu.+ Kenako anabwerera kumsasa wa Isiraeli ndi kuwauza kuti: “Tiyeni,+ pakuti Yehova wapereka msasa wa Amidiyani m’manja mwanu.” 1 Samueli 17:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo mpingo wonsewu udziwa kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga kapena mkondo,+ chifukwa Yehova ndiye mwini nkhondo,+ moti apereka anthu inu m’manja mwathu.”+
15 Gidiyoni atangomva lotolo ndi tanthauzo lake,+ analambira Mulungu.+ Kenako anabwerera kumsasa wa Isiraeli ndi kuwauza kuti: “Tiyeni,+ pakuti Yehova wapereka msasa wa Amidiyani m’manja mwanu.”
47 Ndipo mpingo wonsewu udziwa kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga kapena mkondo,+ chifukwa Yehova ndiye mwini nkhondo,+ moti apereka anthu inu m’manja mwathu.”+