2 Mbiri 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu okhala mu Yerusalemu, ndi inu Mfumu Yehosafati! Izi n’zimene Yehova wanena kwa inu, ‘Musaope+ kapena kuchita mantha ndi khamu lalikululi, popeza nkhondoyi si yanu ndi ya Mulungu.+ Salimo 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.] Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+
15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu okhala mu Yerusalemu, ndi inu Mfumu Yehosafati! Izi n’zimene Yehova wanena kwa inu, ‘Musaope+ kapena kuchita mantha ndi khamu lalikululi, popeza nkhondoyi si yanu ndi ya Mulungu.+
11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]