Genesis 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa linali litatuluka pamene Yakobo anali kuchoka pa Penueli, koma anali kuyenda chotsimphina.+ 1 Mafumu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yerobowamu anamanga mzinda wa Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, n’kuyamba kukhala kumeneko. Kenako anachoka kumeneko n’kupita kukamanga mzinda wa Penueli.+
25 Yerobowamu anamanga mzinda wa Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, n’kuyamba kukhala kumeneko. Kenako anachoka kumeneko n’kupita kukamanga mzinda wa Penueli.+