Oweruza 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno zinachitika kuti Gidiyoni atangomwalira, ana a Isiraeli anayambanso kupembedza Abaala,+ moti anaika Baala-beriti* kukhala mulungu wawo.+ Oweruza 9:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Nzika zonse za munsanja ya Sekemu zitamva nkhani imeneyi, nthawi yomweyo zinalowa m’chipinda chotetezeka cha m’nyumba ya Eli-beriti.*+
33 Ndiyeno zinachitika kuti Gidiyoni atangomwalira, ana a Isiraeli anayambanso kupembedza Abaala,+ moti anaika Baala-beriti* kukhala mulungu wawo.+
46 Nzika zonse za munsanja ya Sekemu zitamva nkhani imeneyi, nthawi yomweyo zinalowa m’chipinda chotetezeka cha m’nyumba ya Eli-beriti.*+