Numeri 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi n’kuyamba kukhala m’mizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni,+ ndi m’midzi yake yonse yozungulira. Salimo 135:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+
25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi n’kuyamba kukhala m’mizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni,+ ndi m’midzi yake yonse yozungulira.
11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+