Luka 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale akuchimwire maulendo 7 pa tsiku, n’kubwera kwa iwe maulendo 7, kudzanena kuti, ‘Ndalapa ine,’ umukhululukire ndithu.”+
4 Ngakhale akuchimwire maulendo 7 pa tsiku, n’kubwera kwa iwe maulendo 7, kudzanena kuti, ‘Ndalapa ine,’ umukhululukire ndithu.”+