Genesis 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova+ anakapeza Hagara m’chipululu ali pakasupe wamadzi wa panjira yopita ku Shura.+ Luka 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye, ataimirira kudzanja lamanja la guwa lansembe zofukiza.+
7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova+ anakapeza Hagara m’chipululu ali pakasupe wamadzi wa panjira yopita ku Shura.+