Machitidwe 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsiku lina cha m’ma 3 koloko masana,*+ anaona mngelo+ wa Mulungu m’masomphenya.+ Mngeloyo anabwera kwa iye n’kunena kuti: “Koneliyo!”
3 Tsiku lina cha m’ma 3 koloko masana,*+ anaona mngelo+ wa Mulungu m’masomphenya.+ Mngeloyo anabwera kwa iye n’kunena kuti: “Koneliyo!”