Genesis 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova+ anakapeza Hagara m’chipululu ali pakasupe wamadzi wa panjira yopita ku Shura.+ Genesis 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Hagara anayamba kutchula dzina la Yehova n’kunena kuti: “Inu ndinu Mulungu amene amaona chilichonse.”*+ Anatinso: “Kodi nanenso pano ndaona wotha kundionayo?” Genesis 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Potsirizira pake, Yakobo anatsala yekhayekha. Kenako, munthu winawake anayamba kulimbana naye usiku wonse mpaka m’bandakucha.+ Genesis 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero Yakobo anatcha malowo Penieli,*+ chifukwa iye anati, “Ndaonana ndi Mulungu pamasom’pamaso, komabe ndapulumuka.”+ Ekisodo 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo anawonjezera kuti: “Sungathe kuona nkhope yanga, chifukwa palibe munthu angandione n’kukhalabe ndi moyo.”+ Yohane 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+
7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova+ anakapeza Hagara m’chipululu ali pakasupe wamadzi wa panjira yopita ku Shura.+
13 Ndiyeno Hagara anayamba kutchula dzina la Yehova n’kunena kuti: “Inu ndinu Mulungu amene amaona chilichonse.”*+ Anatinso: “Kodi nanenso pano ndaona wotha kundionayo?”
24 Potsirizira pake, Yakobo anatsala yekhayekha. Kenako, munthu winawake anayamba kulimbana naye usiku wonse mpaka m’bandakucha.+
30 Chotero Yakobo anatcha malowo Penieli,*+ chifukwa iye anati, “Ndaonana ndi Mulungu pamasom’pamaso, komabe ndapulumuka.”+
20 Ndipo anawonjezera kuti: “Sungathe kuona nkhope yanga, chifukwa palibe munthu angandione n’kukhalabe ndi moyo.”+
18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+