Oweruza 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anatengako uchiwo m’manja n’kumadya akuyenda.+ Atapezananso ndi bambo ndi mayi ake, anawagawira uchiwo ndipo iwo anayamba kudya. Iye sanawauze kuti uchiwo wautenga m’thupi la mkango wakufa.
9 Ndiyeno anatengako uchiwo m’manja n’kumadya akuyenda.+ Atapezananso ndi bambo ndi mayi ake, anawagawira uchiwo ndipo iwo anayamba kudya. Iye sanawauze kuti uchiwo wautenga m’thupi la mkango wakufa.