Nyimbo ya Solomo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Anthu inu mutigwirire nkhandwe+ zing’onozing’ono zimene zikuwononga minda ya mpesa, chifukwa minda yathu ya mpesa yachita maluwa.”+ Maliro 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhandwe zayamba kuyendayenda paphiri la Ziyoni chifukwa lasanduka bwinja.+
15 “Anthu inu mutigwirire nkhandwe+ zing’onozing’ono zimene zikuwononga minda ya mpesa, chifukwa minda yathu ya mpesa yachita maluwa.”+