Oweruza 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Samisoni ananyamuka ndi kugwira nkhandwe 300,+ ndipo anatenga nkhandwezo ziwiriziwiri n’kuzimanga michira. Atatero, anaika muuni umodzi pakati penipeni pa michira iwiriyo. Maliro 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhandwe zayamba kuyendayenda paphiri la Ziyoni chifukwa lasanduka bwinja.+
4 Pamenepo Samisoni ananyamuka ndi kugwira nkhandwe 300,+ ndipo anatenga nkhandwezo ziwiriziwiri n’kuzimanga michira. Atatero, anaika muuni umodzi pakati penipeni pa michira iwiriyo.