Genesis 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawiyi n’kuti Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake. Akali kumeneko, Rakele anaba aterafi*+ a bambo ake. Genesis 31:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ngati wachoka chifukwa cholakalaka kwambiri kunyumba kwa bambo ako, nanga n’chifukwa chiyani waba milungu yanga?”+ Oweruza 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mika anali ndi nyumba ya milungu,+ chotero anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake mphamvu,*+ kuti azitumikira monga wansembe wake.+ Hoseya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa masiku ambiri, ana a Isiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe,+ chipilala chopatulika, efodi,+ ndi aterafi.*+
19 Pa nthawiyi n’kuti Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake. Akali kumeneko, Rakele anaba aterafi*+ a bambo ake.
30 Ngati wachoka chifukwa cholakalaka kwambiri kunyumba kwa bambo ako, nanga n’chifukwa chiyani waba milungu yanga?”+
5 Ndiyeno Mika anali ndi nyumba ya milungu,+ chotero anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake mphamvu,*+ kuti azitumikira monga wansembe wake.+
4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa masiku ambiri, ana a Isiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe,+ chipilala chopatulika, efodi,+ ndi aterafi.*+